Mwachiyika pati

Mwachiyika pati

Created by: [email protected]

Music Images

Lyrics / Prompt

Mtenthera!
Tangonyamukabe,poti tili ndi miyendo!
Koma komwe tikupita
Tonse sitikukudziwa!
Ngakhale otsogolera,naye akudabwa
Tili mu mdima tonse!
Amene atenga nyali,
Aziyika mmatumba
Koma tsoka ndi ilo,atiyika kutsogolo!
Chikondi chanu mwachiyika pati
Utsogoleri want mwawuyika pati
Tsogolo lathu mwalisiya pati
Zokhumba zathu mwazisiya pati
Pamaso ndinu angwilo!
Mukamayankhula,ndinu oyera!
Koma tikasiyana mukukoza zanu
Mavuto athu Kwa Inu ndi nthano
Eeeh!mwatiyika pati eeh
Eeh mwatisiya pati eeh
Chikondi chanu mwachiyika pati
Utsogoleri want mwawuyika pati
Tsogolo lathu mwalisiya pati
Zokhumba zathu mwazisiya pati
Chikondi chanu mwachiyika pati
Utsogoleri want mwawuyika pati
Tsogolo lathu mwalisiya pati
Zokhumba zathu mwazisiya pati 

Comments