Mikango yolusa

Mikango yolusa

Created by: [email protected]
jazzrelaxing

Music Images

Lyrics / Prompt

Mtenthera! Eeeeh! kuli mikango yolusa
Ikumandyaso ngakhale Nyerere 
Basi mudzi uno ulakatika
Mmmm Titha basi
kuli mikango yolusa
Ikumandyaso ngakhale Nyerere 
Basi mudzi uno ulakatika
Mmmm Titha basi 
Inabwera mogonja
Ife mwachikondi chanthu
Tinawakhulupilira!
Koma eeeh!lero sinizo
Atichita kanthu!
Pena ndimadzilirira
Kapena mwina chitsiru ndine
 kuli mikango yolusa
Ikumandyaso ngakhale Nyerere 
Basi mudzi uno ulakatika
Mmmm Titha basi
kuli mikango yolusa
Ikumandyaso ngakhale Nyerere 
Basi mudzi uno ulakatika
Mmmm Titha basi
Ankachita kuvetsa chisoni
Ife nkumati uyu ndiye munthu
Koma pano ndiye ativulaza
Pano kalikose atenga
Palipose agwirapo
Atiwona uchitsiru
Tikati tilakhule, chikwanje tichiwona
kuli mikango yolusa
Ikumandyaso ngakhale Nyerere 
Basi mudzi uno ulakatika
Mmmm Titha basi
kuli mikango yolusa
Ikumandyaso ngakhale Nyerere 
Basi mudzi uno ulakatika
Mmmm Titha basi
Inunso a zipembedzo!
Pano Mwalowa nyasi!
Kwanu nkunyenga nkulemera
Za ufumu zija munayiwala
Poti sitikuwona
Tikafusa mukuti nziwanda
Kodi chowonadi mwachiyika pati!
Tatiyankheni
kuli mikango yolusa
Ikumandyaso ngakhale Nyerere 
Basi mudzi uno ulakatika
Mmmm Titha basi
kuli mikango yolusa
Ikumandyaso ngakhale Nyerere 
Basi mudzi uno ulakatika
Mmmm Titha basi
Abale ako pano si anthu!
Azako pano ndizigawenga!
Pano dziko ndi lako lokha
Ukafuna kugawana ndi ena ujiwa!
Umazuzika anthu nkumayimba za iwe!
Pano osamalana naye ndi iwe mwini basi
Odala ndi amene adzikhulupilira
Uli wekha limba!
kuli mikango yolusa
Ikumandyaso ngakhale Nyerere 
Basi mudzi uno ulakatika
Mmmm Titha basi
kuli mikango yolusa
Ikumandyaso ngakhale Nyerere 
Basi mudzi uno ulakatika
Mmmm Titha basi

Comments