Mtenthera! Eeeeh! kuli mikango yolusa Ikumandyaso ngakhale Nyerere Basi mudzi uno ulakatika Mmmm Titha basi kuli mikango yolusa Ikumandyaso ngakhale Nyerere Basi mudzi uno ulakatika Mmmm Titha basi Inabwera mogonja Ife mwachikondi chanthu Tinawakhulupilira! Koma eeeh!lero sinizo Atichita kanthu! Pena ndimadzilirira Kapena mwina chitsiru ndine kuli mikango yolusa Ikumandyaso ngakhale Nyerere Basi mudzi uno ulakatika Mmmm Titha basi kuli mikango yolusa Ikumandyaso ngakhale Nyerere Basi mudzi uno ulakatika Mmmm Titha basi Ankachita kuvetsa chisoni Ife nkumati uyu ndiye munthu Koma pano ndiye ativulaza Pano kalikose atenga Palipose agwirapo Atiwona uchitsiru Tikati tilakhule, chikwanje tichiwona kuli mikango yolusa Ikumandyaso ngakhale Nyerere Basi mudzi uno ulakatika Mmmm Titha basi kuli mikango yolusa Ikumandyaso ngakhale Nyerere Basi mudzi uno ulakatika Mmmm Titha basi Inunso a zipembedzo! Pano Mwalowa nyasi! Kwanu nkunyenga nkulemera Za ufumu zija munayiwala Poti sitikuwona Tikafusa mukuti nziwanda Kodi chowonadi mwachiyika pati! Tatiyankheni kuli mikango yolusa Ikumandyaso ngakhale Nyerere Basi mudzi uno ulakatika Mmmm Titha basi kuli mikango yolusa Ikumandyaso ngakhale Nyerere Basi mudzi uno ulakatika Mmmm Titha basi Abale ako pano si anthu! Azako pano ndizigawenga! Pano dziko ndi lako lokha Ukafuna kugawana ndi ena ujiwa! Umazuzika anthu nkumayimba za iwe! Pano osamalana naye ndi iwe mwini basi Odala ndi amene adzikhulupilira Uli wekha limba! kuli mikango yolusa Ikumandyaso ngakhale Nyerere Basi mudzi uno ulakatika Mmmm Titha basi kuli mikango yolusa Ikumandyaso ngakhale Nyerere Basi mudzi uno ulakatika Mmmm Titha basi