Takulandirani inu nonse.
Mwasonkhana kudzaphunzira
Choonadi chochoka kwa M’lungu.
Iye akaitana timavomera.
2.Tikuyamikira abalewa
Chifukwa amatilandira.
Tiziwasonyezatu chikondi.
Tilandirenso ena odzasonkhana.
3.Aliyense akuitanidwa
Kuti apeze choonadi.
M’lungu watikokera kwa Iye
Choncho tilandirane ndi mtima wonse.